Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 6:9, 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Iye anamuuza kuti, “Pita ukauze anthu awa kuti:

      ‘Mudzamva mobwerezabwereza

      Koma simudzamvetsetsa.

      Mudzaona mobwerezabwereza,

      Koma simudzazindikira chilichonse.’+

      10 Uchititse anthu awa kuumitsa mtima wawo,+

      Uchititse makutu awo kuti asamamve,+

      Ndipo umate maso awo,

      Kuti asamaone ndi maso awowo,

      Ndiponso kuti asamamve ndi makutu awo,

      Nʼcholinga choti mtima wawo usamvetse zinthu

      Komanso kuti asabwerere nʼkuchiritsidwa.”

  • Yeremiya 5:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “Tamverani izi anthu opusa komanso opanda nzeru inu:*+

      Iwo ali ndi maso koma sangathe kuona,+

      Ali ndi makutu koma sangathe kumva.+

  • Aroma 11:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 ngati mmene Malemba amanenera kuti: “Mulungu wawapatsa mzimu wa tulo tofa nato,+ maso osaona ndi makutu osamva, mpaka lero.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena