Ezekieli 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iye anapitiriza kundiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa Aisiraeli,+ ku mitundu ya anthu amene andipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+ Ezekieli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kaya akamvetsera kapena ayi, popeza iwo ndi anthu opanduka,+ adzadziwabe ndithu kuti pakati pawo panali mneneri.+
3 Iye anapitiriza kundiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu, ndikukutumiza kwa Aisiraeli,+ ku mitundu ya anthu amene andipandukira.+ Iwo ndi makolo awo akhala akuphwanya malamulo anga mpaka lero.+
5 Kaya akamvetsera kapena ayi, popeza iwo ndi anthu opanduka,+ adzadziwabe ndithu kuti pakati pawo panali mneneri.+