Yesaya 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zodabwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala mʼphiri la Ziyoni. Ezekieli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Utenge chiwaya ndipo uchiike pakati pa iweyo ndi mzindawo kuti chikhale ngati khoma lachitsulo. Uziyangʼana mzindawo monyansidwa ndipo usonyeze zimene adani adzachite poukira mzindawo. Chimenechi chikhale chizindikiro ku mtundu wa Isiraeli.+ Ezekieli 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ezekieli wakhala chizindikiro kwa inu.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Tsokali likadzakugwerani, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”
18 Taonani, ine ndi ana amene Yehova wandipatsa+ tili ngati zizindikiro+ ndiponso ngati zodabwitsa mu Isiraeli, zochokera kwa Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, amene amakhala mʼphiri la Ziyoni.
3 Utenge chiwaya ndipo uchiike pakati pa iweyo ndi mzindawo kuti chikhale ngati khoma lachitsulo. Uziyangʼana mzindawo monyansidwa ndipo usonyeze zimene adani adzachite poukira mzindawo. Chimenechi chikhale chizindikiro ku mtundu wa Isiraeli.+
24 Ezekieli wakhala chizindikiro kwa inu.+ Mudzachita zonse zimene iye wachita. Tsokali likadzakugwerani, mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”’”