Yeremiya 52:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga ena mwa anthu onyozeka ndiponso anthu ena onse amene anatsala mumzindawo. Anatenganso anthu amene anathawira kwa mfumu ya Babulo komanso amisiri onse aluso nʼkupita nawo ku ukapolo.+
15 Nebuzaradani mkulu wa asilikali olondera mfumu anatenga ena mwa anthu onyozeka ndiponso anthu ena onse amene anatsala mumzindawo. Anatenganso anthu amene anathawira kwa mfumu ya Babulo komanso amisiri onse aluso nʼkupita nawo ku ukapolo.+