Yeremiya 16:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Mʼmasiku anu, ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi mʼmalo ano, inuyo mukuona.’+ Habakuku 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Yangʼanani pakati pa mitundu ya anthu ndipo muyangʼanitsitse. Muyangʼane modabwa. Dabwani ndithu.Chifukwa pali zimene zichitike mʼmasiku anu,Zimene simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+
9 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Mʼmasiku anu, ndidzathetsa phokoso lachikondwerero, phokoso lachisangalalo, mawu a mkwati ndi mawu a mkwatibwi mʼmalo ano, inuyo mukuona.’+
5 Yangʼanani pakati pa mitundu ya anthu ndipo muyangʼanitsitse. Muyangʼane modabwa. Dabwani ndithu.Chifukwa pali zimene zichitike mʼmasiku anu,Zimene simungakhulupirire ngakhale wina atakufotokozerani.+