Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mika 3:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Izi nʼzimene Yehova wanena zomwe zidzachitikire aneneri amene akusocheretsa anthu a mtundu wanga.+

      Amene amalengeza kuti ‘Mtendere!’+ kwinaku akuluma ndi mano awo.*+

      Koma munthu akapanda kuika chakudya mʼkamwa mwawo, amakonzekera zokamenyana naye:

  • Zefaniya 3:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Aneneri ake ndi amwano ndiponso achinyengo.+

      Ansembe ake amaipitsa zinthu zopatulika,+

      Ndipo amaphwanya malamulo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena