Ezekieli 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 ‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala kapena kuima pamalo ogumuka a mpandawo kuti ateteze dzikolo nʼcholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense.
30 ‘Ndinafunafuna munthu pakati pawo amene angathe kukonzanso mpanda wamiyala kapena kuima pamalo ogumuka a mpandawo kuti ateteze dzikolo nʼcholinga choti ine ndisaliwononge,+ koma sindinapeze aliyense.