Yesaya 30:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwo auza anthu oona masomphenya kuti, ‘Lekani kuona masomphenya,’ Ndipo anthu olosera zamʼtsogolo awauza kuti, ‘Musatiuze masomphenya olondola.+ Mutiuze zinthu zotikomera. Muziona masomphenya abodza.+ Ezekieli 22:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Koma aneneri amʼdzikomo apaka laimu zochita za akalongawo. Iwo amaona masomphenya onama ndipo amalosera zinthu zabodza.+ Aneneriwo amanena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.
10 Iwo auza anthu oona masomphenya kuti, ‘Lekani kuona masomphenya,’ Ndipo anthu olosera zamʼtsogolo awauza kuti, ‘Musatiuze masomphenya olondola.+ Mutiuze zinthu zotikomera. Muziona masomphenya abodza.+
28 Koma aneneri amʼdzikomo apaka laimu zochita za akalongawo. Iwo amaona masomphenya onama ndipo amalosera zinthu zabodza.+ Aneneriwo amanena kuti: “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti,” pamene Yehova sananene chilichonse.