Yesaya 27:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Mudzalimbana naye ndi mfuu yoopseza pomuthamangitsa. Iye adzamuthamangitsa ndi mphepo yake yamphamvu pa tsiku lamphepo yakumʼmawa.+
8 Mudzalimbana naye ndi mfuu yoopseza pomuthamangitsa. Iye adzamuthamangitsa ndi mphepo yake yamphamvu pa tsiku lamphepo yakumʼmawa.+