-
Yesaya 30:12, 13Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
12 Choncho Woyera wa Isiraeli wanena kuti:
“Chifukwa chakuti mwakana mawu awa,+
Mukudalira katangale komanso chinyengo
Ndipo mukukhulupirira zinthu zimenezi,+
13 Cholakwa chanuchi chidzakhala ngati mpanda wogumuka kwa inu,
Ngati mpanda wautali umene wapendekeka ndipo watsala pangʼono kugwa.
Udzagwa mwadzidzidzi mʼkanthawi kochepa.
-