Levitiko 26:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ndidzatumiza zilombo zakutchire pakati panu,+ ndipo zidzakupherani ana anu+ ndi ziweto zanu nʼkuchepetsa chiwerengero chanu, moti mʼmisewu yanu mudzakhala mopanda anthu.+ Yeremiya 15:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ndidzawabweretsera masoka okwanira 4,’*+ akutero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, mbalame zamumlengalenga komanso zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.+
22 Ndidzatumiza zilombo zakutchire pakati panu,+ ndipo zidzakupherani ana anu+ ndi ziweto zanu nʼkuchepetsa chiwerengero chanu, moti mʼmisewu yanu mudzakhala mopanda anthu.+
3 “‘Ndidzawabweretsera masoka okwanira 4,’*+ akutero Yehova. ‘Ndidzawatumizira lupanga kuti liwaphe, agalu kuti akoke mitembo yawo, mbalame zamumlengalenga komanso zilombo zakutchire kuti ziwadye ndi kuwawononga.+