Zefaniya 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Ndidzasesa anthu ndi nyama. Ndidzasesa mbalame zamumlengalenga ndiponso nsomba zamʼnyanja.+Ndidzasesanso zopunthwitsa*+ pamodzi ndi anthu oipa,Ndipo ndidzawononga anthu onse padziko,” watero Yehova.
3 “Ndidzasesa anthu ndi nyama. Ndidzasesa mbalame zamumlengalenga ndiponso nsomba zamʼnyanja.+Ndidzasesanso zopunthwitsa*+ pamodzi ndi anthu oipa,Ndipo ndidzawononga anthu onse padziko,” watero Yehova.