Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 1:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Ndiyeno Yehova anafunsanso Satana kuti: “Kodi mtima wako uli pa mtumiki wanga Yobu? Padziko lapansi palibe wina wofanana naye. Iye ndi munthu wokhulupirika amene amachita zoyenera,*+ amaopa Mulungu ndiponso amapewa zoipa.”

  • Yobu 42:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Tsopano utenge ngʼombe zamphongo 7 ndi nkhosa zamphongo 7. Upite nazo kwa mtumiki wanga Yobu, ndipo inuyo mukapereke nsembe yopsereza chifukwa cha tchimo lanu. Ndiyeno Yobu mtumiki wanga akakupemphererani.+ Ndithudi ineyo ndidzayankha pempho lake* kuti ndisakuchitireni zinthu mogwirizana ndi zopusa zimene mwachita, chifukwa simunanene zoona zokhudza ine ngati mmene wachitira mtumiki wanga Yobu.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena