Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 18:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Moyo umene ukuchimwawo ndi umene udzafe.*+ Mwana sadzakhala ndi mlandu uliwonse pa zolakwa za bambo ake ndipo bambo sadzakhala ndi mlandu uliwonse pa zolakwa za mwana wake. Munthu wolungama adzaweruzidwa yekha mogwirizana ndi zinthu zachilungamo zimene amachita, ndipo munthu woipa adzaweruzidwa yekha mogwirizana ndi zinthu zoipa zimene amachita.+

  • Zefaniya 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Funafunani Yehova,+ inu nonse ofatsa* apadziko lapansi,

      Amene mumatsatira malamulo ake olungama.*

      Yesetsani kukhala olungama, yesetsani kukhala ofatsa.*

      Mwina mungadzabisike pa tsiku la mkwiyo wa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena