Ezekieli 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthu amene aphedwa adzagwa pakati panu,+ ndipo inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.+ Ezekieli 7:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Diso langa silidzakumvera chisoni ndipo sindidzakuchitira chifundo.+ Ndidzakulanga mogwirizana ndi njira zako, moti udzakumana ndi mavuto chifukwa cha zinthu zonyansa zimene ukuchita.+ Udzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+
4 Diso langa silidzakumvera chisoni ndipo sindidzakuchitira chifundo.+ Ndidzakulanga mogwirizana ndi njira zako, moti udzakumana ndi mavuto chifukwa cha zinthu zonyansa zimene ukuchita.+ Udzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+