2 Mbiri 36:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Anthu ndi atsogoleri onse a ansembe anali osakhulupirika ngakhale pangʼono ndipo ankachita zonyansa zonse zimene anthu a mitundu ina ankachita. Iwo anaipitsa nyumba ya Yehova+ imene iye anaiyeretsa ku Yerusalemu.
14 Anthu ndi atsogoleri onse a ansembe anali osakhulupirika ngakhale pangʼono ndipo ankachita zonyansa zonse zimene anthu a mitundu ina ankachita. Iwo anaipitsa nyumba ya Yehova+ imene iye anaiyeretsa ku Yerusalemu.