-
Ezekieli 3:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Mzimu unandinyamula nʼkupita nane ndili wachisoni komanso wokwiya kwambiri. Dzanja la Yehova linandigwira mwamphamvu.
-