Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 16:51
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 51 Komanso Samariya+ sanachite machimo ofika ngakhale hafu ya machimo ako. Koma iwe unapitiriza kuchulukitsa zinthu zonyansa zimene unkachita kuposa abale ako, moti unachititsa kuti azichemwali ako aoneke ngati olungama chifukwa cha zinthu zonse zonyansa zimene unkachita.+

  • Ezekieli 22:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 “Iwe mwana wa munthu, kodi ndiwe wokonzeka kupereka uthenga wachiweruzo kwa mzinda* umene uli ndi mlandu wa magaziwu+ komanso kuudziwitsa zonyansa zake zonse?+

  • Luka 11:47
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 47 Tsoka kwa inu, chifukwa mumamanga manda* a aneneri, komatu makolo anu ndi amene anawapha!+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena