Ekisodo 3:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho ndipita kuti ndikawapulumutse mʼmanja mwa Aiguputo+ ndi kuwatulutsa mʼdzikolo nʼkuwalowetsa mʼdziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+
8 Choncho ndipita kuti ndikawapulumutse mʼmanja mwa Aiguputo+ ndi kuwatulutsa mʼdzikolo nʼkuwalowetsa mʼdziko labwino komanso lalikulu, dziko loyenda mkaka ndi uchi.+ Ndiwalowetsa mʼdziko la Akanani, Ahiti, Aamori, Aperezi, Ahivi ndi Ayebusi.+