Salimo 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Chifukwa cha dzina lanu, inu Yehova,+Mundikhululukire tchimo langa, ngakhale kuti ndi lalikulu. Salimo 79:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tithandizeni inu Mulungu amene mumatipulumutsa,+Chifukwa cha dzina lanu laulemerero.Tipulumutseni komanso mutikhululukire* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+ Yeremiya 14:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ngakhale kuti machimo athu akuchitira umboni kuti ndife olakwa,Inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu.+ Chifukwa zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika nʼzambiri,+Ndipo takuchimwirani. Danieli 9:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Imvani, inu Yehova. Tikhululukireni,+ inu Yehova. Timvereni ndipo muchitepo kanthu, inu Yehova! Musazengereze inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu. Chifukwa mzinda wanu ndi anthu anu amadziwika ndi dzina lanu.”+
9 Tithandizeni inu Mulungu amene mumatipulumutsa,+Chifukwa cha dzina lanu laulemerero.Tipulumutseni komanso mutikhululukire* machimo athu chifukwa cha dzina lanu.+
7 Ngakhale kuti machimo athu akuchitira umboni kuti ndife olakwa,Inu Yehova, chitanipo kanthu chifukwa cha dzina lanu.+ Chifukwa zochita zathu zosonyeza kusakhulupirika nʼzambiri,+Ndipo takuchimwirani.
19 Imvani, inu Yehova. Tikhululukireni,+ inu Yehova. Timvereni ndipo muchitepo kanthu, inu Yehova! Musazengereze inu Mulungu wanga, chifukwa cha dzina lanu. Chifukwa mzinda wanu ndi anthu anu amadziwika ndi dzina lanu.”+