Levitiko 26:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+ Salimo 106:26, 27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,Kuti adzachititsa kuti afere mʼchipululu.+27 Adzachititsa kuti mbadwa zawo ziphedwe ndi anthu a mitundu ina,Ndiponso kuwamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+
33 Ine ndidzakubalalitsani pakati pa anthu a mitundu ina,+ ndipo ndidzakusololerani lupanga ndi kukuthamangitsani.+ Dziko lanu lidzakhala bwinja, ndipo mizinda yanu idzawonongedwa.+
26 Choncho Mulungu anawalumbirira atakweza dzanja lake,Kuti adzachititsa kuti afere mʼchipululu.+27 Adzachititsa kuti mbadwa zawo ziphedwe ndi anthu a mitundu ina,Ndiponso kuwamwaza mʼmayiko osiyanasiyana.+