Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuchita zofuna za mtima wawo wosamverawo.Iwo anachita zimene ankaganiza kuti nʼzoyenera.*+
12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuchita zofuna za mtima wawo wosamverawo.Iwo anachita zimene ankaganiza kuti nʼzoyenera.*+