-
Yeremiya 13:26, 27Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Choncho ndidzakuvula siketi yako nʼkukuphimba nayo kumaso,
Ndipo anthu adzaona maliseche ako.+
27 Chigololo chimene ukuchita,+ kumemesa* kwako,
Khalidwe lako lonyansa* la uhule, zonsezi zidzaonekera.
Ndaona khalidwe lako lonyansa+
Mʼmapiri komanso kuthengo.
Tsoka kwa iwe Yerusalemu!
Kodi ukhalabe wodetsedwa mpaka liti?”+
-