Yeremiya 21:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ine ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima komanso ndili ndi ukali waukulu.+ Ezekieli 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Choncho ineyo ndidzawalanga nditakwiya kwambiri. Diso langa silidzawamvera chisoni ndipo sindidzawachitira chifundo.+ Ngakhale iwo adzandilirire mofuula, ine sindidzamva.”+
5 Ine ndidzamenyana nanu+ ndi mkono wotambasula ndiponso dzanja lamphamvu. Ndidzachita zimenezi nditakwiya, nditapsa mtima komanso ndili ndi ukali waukulu.+
18 Choncho ineyo ndidzawalanga nditakwiya kwambiri. Diso langa silidzawamvera chisoni ndipo sindidzawachitira chifundo.+ Ngakhale iwo adzandilirire mofuula, ine sindidzamva.”+