Oweruza 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pitani, mukapemphe thandizo kwa milungu imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyoyo ikupulumutseni pa nthawi imene mukuvutikayi.”+ Salimo 81:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuchita zofuna za mtima wawo wosamverawo.Iwo anachita zimene ankaganiza kuti nʼzoyenera.*+
14 Pitani, mukapemphe thandizo kwa milungu imene mwasankhayo.+ Milungu imeneyoyo ikupulumutseni pa nthawi imene mukuvutikayi.”+
12 Choncho ndinawasiya kuti apitirize kuchita zofuna za mtima wawo wosamverawo.Iwo anachita zimene ankaganiza kuti nʼzoyenera.*+