2 Mbiri 7:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ineyo ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga. Ndidzachititsa anthu kuinyoza ndiponso kuinenera mawu achipongwe pakati pa mitundu yonse ya anthu.+ Maliro 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wachita zimene ankafuna.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wakuwononga mopanda chisoni.+ Wachititsa kuti adani ako asangalale chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wawonjezera mphamvu* za adani ako.
20 ineyo ndidzachotsa Aisiraeli mʼdziko limene ndawapatsa+ ndipo nyumba iyi yomwe ndaiyeretsa chifukwa cha dzina langa, ndidzaichotsa pamaso panga. Ndidzachititsa anthu kuinyoza ndiponso kuinenera mawu achipongwe pakati pa mitundu yonse ya anthu.+
17 Yehova wachita zimene ankafuna.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wakuwononga mopanda chisoni.+ Wachititsa kuti adani ako asangalale chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wawonjezera mphamvu* za adani ako.