Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 28:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Aedomu anabweranso nʼkudzaukira Ayuda ndipo anagwira anthu nʼkuwatenga.

  • Salimo 137:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  7 Inu Yehova, kumbukirani

      Zimene Aedomu ananena pa tsiku limene Yerusalemu anawonongedwa.

      Iwo anati: “Gwetsani mzindawo! Ugwetseni mpaka pamaziko ake!”+

  • Maliro 4:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iwe mwana wamkazi wa Ziyoni,* chilango chimene anakupatsa chifukwa cha zolakwa zako chatha.

      Sadzakutenganso kupita nawe ku ukapolo.+

      Koma Mulungu adzatembenukira kwa iwe, mwana wamkazi wa Edomu, kuti aone zolakwa zako.

      Machimo ako adzawaika poyera.+

  • Amosi 1:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Yehova wanena kuti,

      ‘Chifukwa Edomu wandigalukira mobwerezabwereza,+ sindidzamusinthira chigamulo changa.

      Chifukwa anathamangitsa mʼbale wake ndi lupanga,+

      Komanso anakana kusonyeza chifundo.

      Anapitiriza kuwakhadzulakhadzula,

      Ndipo anapitirizabe kuwakwiyira kwambiri.+

  • Obadiya 10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Popeza unachitira nkhanza mʼbale wako Yakobo,+

      Udzachititsidwa manyazi kwambiri.+

      Udzaphedwa ndipo sudzakhalaponso mpaka kalekale.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena