Yeremiya 25:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+ Yeremiya 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 ndiponso anthu a mitundu yosiyanasiyana. Mafumu onse amʼdziko la Uzi, mafumu onse amʼdziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza, Ekironi komanso amene anatsala ku Asidodi, Zefaniya 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Gaza adzakhala mzinda wosiyidwa,Ndipo Asikeloni adzakhala bwinja.+ Anthu a ku Asidodi adzathamangitsidwa dzuwa likuswa mtengo,*Ndipo Ekironi adzazulidwa.+
17 Choncho ndinatenga kapu imene inali mʼdzanja la Yehova ndipo ndinamwetsa mitundu yonse imene Yehova ananditumizako. Mitunduyo ndi iyi:+
20 ndiponso anthu a mitundu yosiyanasiyana. Mafumu onse amʼdziko la Uzi, mafumu onse amʼdziko la Afilisiti,+ Asikeloni,+ Gaza, Ekironi komanso amene anatsala ku Asidodi,
4 Gaza adzakhala mzinda wosiyidwa,Ndipo Asikeloni adzakhala bwinja.+ Anthu a ku Asidodi adzathamangitsidwa dzuwa likuswa mtengo,*Ndipo Ekironi adzazulidwa.+