Zefaniya 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Tsoka kwa anthu okhala mʼmbali mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, ndidzakuwononga,Moti mʼdziko lako simudzatsala munthu aliyense.
5 “Tsoka kwa anthu okhala mʼmbali mwa nyanja, mtundu wa Akereti.+ Yehova wakudzudzulani. Iwe Kanani, dziko la Afilisiti, ndidzakuwononga,Moti mʼdziko lako simudzatsala munthu aliyense.