Danieli 2:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Inuyo mfumu yomwe ndi mfumu ya mafumu, amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu ndi ulemerero,
37 Inuyo mfumu yomwe ndi mfumu ya mafumu, amene Mulungu wakumwamba wakupatsani ufumu,+ mphamvu ndi ulemerero,