-
Ezekieli 26:4, 5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Mayikowo adzagwetsa mipanda ya Turo komanso kugumula nsanja zake.+ Ine ndidzapala dothi lake nʼkumusandutsa thanthwe losalala lopanda kanthu. 5 Iye adzakhala malo oyanikapo makoka pakati pa nyanja.’+
‘Ine ndanena ndipo anthu a mitundu ina adzalanda zinthu zake,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
-