Ezekieli 26:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Iwo adzakuimbira nyimbo yoimba polira.+ Azidzati: “Iwe mzinda wotamandika, zoona wawonongekadi!+ Mwa iwe munkakhala anthu ochokera kunyanja.Iwe ndi anthu ako munali amphamvu panyanja,+Munkachititsa mantha anthu onse okhala padziko lapansi.
17 Iwo adzakuimbira nyimbo yoimba polira.+ Azidzati: “Iwe mzinda wotamandika, zoona wawonongekadi!+ Mwa iwe munkakhala anthu ochokera kunyanja.Iwe ndi anthu ako munali amphamvu panyanja,+Munkachititsa mantha anthu onse okhala padziko lapansi.