Genesis 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana a Yafeti anali Gomeri,+ Magogi,+ Madai, Yavani, Tubala,+ Meseki+ ndi Tirasi.+ Genesis 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ana a Yavani anali Elisha,+ Tarisi,+ Kitimu+ ndi Dodanimu.