Yoswa 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Madera amene atsala ndi awa:+ Madera onse a Afilisiti ndi madera onse a Agesuri.+ Yoswa 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 dera la Agebala+ ndiponso dera lonse la Lebanoni chakumʼmawa, kuyambira ku Baala-gadi mʼmunsi mwa phiri la Herimoni mpaka ku Lebo-hamati.*+
5 dera la Agebala+ ndiponso dera lonse la Lebanoni chakumʼmawa, kuyambira ku Baala-gadi mʼmunsi mwa phiri la Herimoni mpaka ku Lebo-hamati.*+