Yeremiya 8:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+
22 Kodi mu Giliyadi mulibe mafuta a basamu?+ Kapena kodi mulibe wochiritsa* mmenemo?+ Nʼchifukwa chiyani mwana wamkazi wa anthu anga sanachiritsidwe?+