1 Mafumu 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ zomwe zinkayenda panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko. Yesaya 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Lirani mofuula, inu sitima zapamadzi za ku Tarisi,Chifukwa malo anu otetezeka awonongedwa.+
22 Zinali choncho chifukwa mfumuyo inali ndi zombo za ku Tarisi+ zomwe zinkayenda panyanja pamodzi ndi zombo za Hiramu. Kamodzi pa zaka zitatu zilizonse, zombozo zinkabweretsa golide, siliva, minyanga ya njovu,+ anyani ndi mbalame zotchedwa pikoko.