Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 27:10, 11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Amuna a ku Perisiya, ku Ludi ndi ku Puti+ anali mʼgulu lako lankhondo, anali mʼgulu la asilikali ako.

      Iwo ankapachika zishango ndi zipewa zawo pamakoma ako ndipo anakubweretsera ulemerero.

      11 Amuna a ku Arivadi amene ali mʼgulu la asilikali ako anaima pamwamba pa mpanda wako kuzungulira mzinda wonse,

      Ndipo amuna olimba mtima ankalondera nsanja zako.

      Iwo anapachika zishango zawo zozungulira mʼmakoma kuzungulira mpanda wako wonse,

      Ndipo anachititsa kuti ukhale wokongola kwambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena