Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 36:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ukudalira thandizo la Iguputo, bango lophwanyika loti munthu ataligwira kuti alitsamire, lingamucheke mʼmanja. Ndi mmene zilili ndi Farao mfumu ya Iguputo kwa onse omudalira.+

  • Yeremiya 37:5-7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndiyeno asilikali a Farao anabwera kuchokera ku Iguputo+ ndipo Akasidi amene anali atazungulira mzinda wa Yerusalemu atamva zimenezi anachoka ku Yerusalemu.+ 6 Kenako Yehova anauza mneneri Yeremiya kuti: 7 “Yehova Mulungu wa Isiraeli wanena kuti, ‘Mfumu ya Yuda imene yakutumani kudzafunsira kwa ine mukaiuze kuti: “Taonani! Asilikali a Farao amene akubwera kudzakuthandizani adzabwerera kwawo ku Iguputo.+

  • Ezekieli 17:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Gulu lalikulu la asilikali komanso asilikali ambirimbiri a Farao sadzamuthandiza pankhondo,+ adani akadzamanga malo okwera omenyerapo nkhondo ndiponso mpanda womenyerapo nkhondo nʼcholinga chakuti aphe anthu ambiri.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena