Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 25:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 ndikuitana mafuko onse akumpoto,”+ akutero Yehova, “ndikuitananso Mfumu Nebukadinezara* ya ku Babulo, mtumiki wanga.+ Ndibweretsa anthu amenewa kuti aukire dziko lino+ ndi anthu amene akukhala mmenemo komanso mitundu yonse imene yakuzungulirani.+ Ndidzakuwonongani inuyo ndi mitundu yonse yokuzungulirani ndipo ndidzakusandutsani chinthu chochititsa mantha chimene anthu azidzachiimbira mluzu ndipo malo anu adzakhala mabwinja mpaka kalekale.

  • Yeremiya 27:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Kenako uzitumize kwa mfumu ya Edomu,+ mfumu ya Mowabu,+ mfumu ya Aamoni,+ mfumu ya Turo+ ndi mfumu ya Sidoni.+ Upatsire amithenga amene abwera ku Yerusalemu kudzaonana ndi Zedekiya mfumu ya Yuda.

  • Yeremiya 27:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa mʼmanja mwa mtumiki wanga, Mfumu Nebukadinezara+ ya ku Babulo. Ndamupatsanso ngakhale nyama zakutchire kuti zimutumikire.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena