-
Ezekieli 30:9, 10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Pa tsikulo, ndidzatumiza amithenga pasitima zapamadzi kuti akaopseze Itiyopiya yemwe ndi wodzidalira. Itiyopiya adzachita mantha kwambiri pa tsiku limene Iguputo adzawonongedwe, chifukwa tsikulo lidzafika ndithu.’
10 Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: ‘Ndidzawononga magulu a anthu a ku Iguputo pogwiritsa ntchito dzanja la Nebukadinezara,* mfumu ya Babulo.+
-