Ezekieli 32:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndikadzakuzimitsa, ndidzaphimba kumwamba nʼkuchititsa mdima nyenyezi zake. Dzuwa ndidzaliphimba ndi mitambo,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.+
7 Ndikadzakuzimitsa, ndidzaphimba kumwamba nʼkuchititsa mdima nyenyezi zake. Dzuwa ndidzaliphimba ndi mitambo,Ndipo mwezi sudzaonetsa kuwala kwake.+