8 Kodi iwe uli pabwino kuposa No-amoni+ amene anali pafupi ndi ngalande zochokera mumtsinje wa Nailo?+
Iye anazunguliridwa ndi madzi.
Nyanja inali chuma chake ndiponso khoma lake.
9 Mphamvu zake zopanda malire zinkachokera ku Itiyopiya ndi ku Iguputo.
Anthu a ku Puti+ ndi a ku Libiya ankamuthandiza.+