-
Ezekieli 32:11, 12Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Chifukwa Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti:
‘Lupanga la mfumu ya Babulo lidzakuukira.+
12 Ndidzachititsa kuti gulu la anthu amene amakutsatira aphedwe ndi malupanga a asilikali amphamvu.
Onsewo ndi anthu a mitundu ina omwe ndi ankhanza kwambiri.+
Iwo adzawononga zinthu zimene Iguputo amazinyadira ndipo anthu ambiri amene amamutsatira adzaphedwa.+
-