Ezekieli 30:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yehova wanena kuti: ‘Anthu amene akuthandiza Iguputo nawonso adzaphedwa,Ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga mʼdzikolo kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. Ezekieli 32:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Farao adzaona zinthu zonsezi ndipo mtima wake udzakhala mʼmalo chifukwa cha zonse zimene zinachitikira gulu la anthu amene ankamutsatira.+ Farao ndi asilikali ake onse adzaphedwa ndi lupanga,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
6 Yehova wanena kuti: ‘Anthu amene akuthandiza Iguputo nawonso adzaphedwa,Ndipo mphamvu zimene amazinyadira zidzatha.+ Anthu adzaphedwa ndi lupanga mʼdzikolo kuchokera ku Migidoli+ mpaka ku Seyene,’+ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.
31 Farao adzaona zinthu zonsezi ndipo mtima wake udzakhala mʼmalo chifukwa cha zonse zimene zinachitikira gulu la anthu amene ankamutsatira.+ Farao ndi asilikali ake onse adzaphedwa ndi lupanga,’ akutero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.