-
Ezekieli 31:9Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
9 Mtengo umenewu ndinaukongoletsa pouchulukitsira masamba,
Ndipo mitengo ina yonse ya mu Edeni, munda wa Mulungu woona, inkauchitira nsanje.’
-
-
Ezekieli 32:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 ‘Kodi ndiwe wokongola kuposa ndani? Tsikira kumanda ndipo ukagone limodzi ndi anthu osadulidwa.
-