Genesis 10:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Ana a Semu anali Elamu,+ Ashuri,+ Aripakisadi,+ Ludi ndi Aramu.+ Yeremiya 49:34, 35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Yehova anauza Yeremiya mawu okhudza Elamu+ kumayambiriro kwa ulamuliro wa Mfumu Zedekiya+ ya Yuda kuti: 35 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ine ndikuthyola uta wa Aelamu,+ umene umachititsa kuti akhale amphamvu.*
34 Yehova anauza Yeremiya mawu okhudza Elamu+ kumayambiriro kwa ulamuliro wa Mfumu Zedekiya+ ya Yuda kuti: 35 “Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti, ‘Ine ndikuthyola uta wa Aelamu,+ umene umachititsa kuti akhale amphamvu.*