Genesis 10:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ana a Yafeti anali Gomeri,+ Magogi,+ Madai, Yavani, Tubala,+ Meseki+ ndi Tirasi.+ Ezekieli 38:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana Gogi wa kudziko la Magogi,+ mtsogoleri wamkulu* wa Meseki ndi Tubala+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzamuchitikire.+
2 “Iwe mwana wa munthu, yangʼana Gogi wa kudziko la Magogi,+ mtsogoleri wamkulu* wa Meseki ndi Tubala+ ndipo ulosere zoipa zimene zidzamuchitikire.+