-
Yeremiya 9:25, 26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Yehova wanena kuti, “Taona masiku akubwera ndipo ndidzaimba mlandu aliyense wodulidwa koma amene sanachite mdulidwe wa mtima wake.+ 26 Ndidzaimba mlandu Iguputo,+ Yuda,+ Edomu,+ Aamoni+ ndi Mowabu+ komanso onse odulira ndevu zawo zamʼmbali amene amakhala mʼchipululu.+ Chifukwa mitundu yonse ndi yosadulidwa ndipo anthu onse a mʼnyumba ya Isiraeli sanachite mdulidwe wa mitima yawo.”+
-