-
Danieli 11:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Zimene ndikufotokozere panopa ndi zoona:
Mu ufumu wa Perisiya mudzakhala mafumu atatu amene adzalamulire, ndipo mfumu ya nambala 4 idzasonkhanitsa chuma chambiri kuposa ena onsewa. Ndipo ikadzangokhala yamphamvu chifukwa cha chuma chakecho, idzagwiritsa ntchito chilichonse pomenyana ndi ufumu wa Girisi.+
-