Danieli 8:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ndiyeno ineyo Danieli ndinatopa kwambiri ndipo ndinadwala kwa masiku angapo.+ Kenako ndinadzuka nʼkugwira ntchito imene mfumu inandipatsa.+ Koma ndinadabwa kwambiri ndi zimene ndinaona ndipo palibe amene akanazimvetsa.+
27 Ndiyeno ineyo Danieli ndinatopa kwambiri ndipo ndinadwala kwa masiku angapo.+ Kenako ndinadzuka nʼkugwira ntchito imene mfumu inandipatsa.+ Koma ndinadabwa kwambiri ndi zimene ndinaona ndipo palibe amene akanazimvetsa.+